
Ine sindikuchoka m’boma-Chakwera
Mtsogoleli wa dziko lino Dr. Lazarus Chakwera wanenetsa kuti sachoka m’boma kudzera pa zisankho za pa 16 September. Dr. Chakwera ati salola kuti anthu omwe amaba ndalama ku Reserve Bank komanso ku nyumba zaboma kuti abwelelenso m’boma. Iwo anena izi pomwe …